-
Numeri 21:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Kenako Mose anatumiza anthu ena kuti akazonde mzinda wa Yazeri.+ Atatero, Aisiraeliwo analanda midzi yozungulira mzindawo, nʼkuthamangitsa Aamori amene anali kumeneko.
-