-
Oweruza 8:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Gidiyoni anapitirizabe ulendo wake ndipo anadutsa njira ya anthu okhala mʼmatenti, kumʼmawa kwa Noba ndi Yogebeha+ ndipo anaukira msasa wa adaniwo iwo asanakonzekere.
-