- 
	                        
            
            Numeri 13:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        26 Iwo anabwerera kwa Mose ndi Aroni ndiponso gulu lonse la Aisiraeli mʼchipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera gulu lonselo za ulendo wawo nʼkuwaonetsa zipatso za kudzikolo. 
 
- 
                                        
- 
	                        
            
            Numeri 32:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        8 Nʼzimenenso makolo anu anachita ku Kadesi-barinea, nditawatuma kuti akafufuze dziko.+ 
 
-