-
Numeri 22:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kenako Aisiraeli ananyamuka nʼkukamanga msasa mʼchipululu cha Mowabu, moyangʼanizana ndi Yeriko patsidya pa mtsinje wa Yorodano.+
-
-
Numeri 36:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Amenewa ndi malamulo ndi zigamulo za Yehova, zimene anapereka kwa Aisiraeli kudzera mwa Mose ku Yeriko, mʼchipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano.+
-