-
Levitiko 5:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Munthu akachimwa pochita chimodzi mwa zinthu zimene Yehova analamula kuti asachite, ngakhale kuti anachita mosazindikira, wapalamulabe mlandu ndipo aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho.+
-