-
Numeri 6:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Tsopano lamulo lokhudza Mnaziri ndi ili: Pa tsiku limene masiku a unaziri+ wake atha, azimubweretsa pakhomo la chihema chokumanako.
-
-
Numeri 6:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Kenako Mnaziriyo azimeta tsitsi lakumutu kwake+ ndipo azimetera pakhomo la chihema chokumanako. Akatero, azitenga tsitsi lakumutu kwake limene linamera pa nthawi yomwe anali Mnaziri, nʼkuliponya pamoto umene uli pansi pa nsembe yamgwirizano.
-