Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ekisodo 25:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Ekisodo 25:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • 1 Mbiri 28:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anamupatsanso mapulani a kamangidwe ka zonse zimene anauzidwa kudzera mwa mzimu zokhudza mabwalo+ a nyumba ya Yehova, zipinda zonse zodyera kuzungulira kachisi, mosungira chuma cha nyumba ya Mulungu woona ndi mosungira zinthu zimene anaziyeretsa kuti zikhale zopatulika.+

  • 1 Mbiri 28:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Davide anati: “Dzanja la Yehova linali pa ine ndipo anandithandiza kuti ndidziwe zonse zokhudza mapulani a kamangidwe kake+ nʼkuwalemba.”+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani