-
Numeri 3:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mabanja a Agerisoni ankamanga misasa yawo kumbuyo kwa chihema,+ mbali yakumadzulo.
-
-
Numeri 3:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Mabanja a ana a Kohati ankamanga msasa wawo kumʼmwera kwa chihema.+
-
-
Numeri 3:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Mtsogoleri wa nyumba ya mabanja a Merari anali Zuriyeli, mwana wa Abihaili. Iwo ankamanga msasa wawo kumpoto kwa chihema.+
-