-
2 Mafumu 2:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ana a aneneri amene anali ku Yeriko atamuona chapatali, ananena kuti: “Tsopano mzimu umene unali ndi Eliya uli ndi Elisa.”+ Choncho anapita kukakumana naye ndipo anamugwadira mpaka nkhope zawo kufika pansi.
-