- 
	                        
            
            Salimo 78:26, 27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        26 Anachititsa kuti mphepo yakumʼmawa iwombe mumlengalenga, Komanso ndi mphamvu zake, anachititsa kuti mphepo yakumʼmwera iwombe.+ 27 Iye anawagwetsera nyama yochuluka ngati fumbi, Anawagwetsera mbalame zochuluka ngati mchenga wamʼmbali mwa nyanja. 
 
-