2 Mbiri 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Uziya, amene anali atanyamula choperekera nsembe, anawakwiyira kwambiri+ ansembewo. Zitatero, anachita khate+ pachipumi pake. Anachita khatelo ansembewo ali pompo mʼnyumba ya Yehova pafupi ndi guwa lansembe zofukiza.
19 Koma Uziya, amene anali atanyamula choperekera nsembe, anawakwiyira kwambiri+ ansembewo. Zitatero, anachita khate+ pachipumi pake. Anachita khatelo ansembewo ali pompo mʼnyumba ya Yehova pafupi ndi guwa lansembe zofukiza.