- 
	                        
            
            Nehemiya 9:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        25 Iwo analanda mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri+ ndi dziko la nthaka yachonde.+ Ndipo anatenga zitsime zokumba kale, nyumba zodzaza ndi zinthu zabwino, minda ya mpesa, minda ya maolivi+ ndiponso mitengo yokhala ndi zipatso zambiri. Choncho ankadya nʼkukhuta moti ananenepa ndipo ankasangalala ndi ubwino wanu waukulu. 
 
-