-
Numeri 13:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Powatumiza kuti akazonde dziko la Kanani, Mose anawauza kuti: “Mupite kumeneko kudzera ku Negebu, ndipo kenako mukafike kudera lamapiri.+
-