32 Ngakhale kuti anakuchitirani zonsezi, simunakhulupirire Yehova Mulungu wanu,+ 33 amene ankayenda patsogolo panu kuti akufufuzireni malo oti mumangepo msasa. Usiku ankakutsogolerani ndi moto ndipo masana ankakutsogolerani ndi mtambo kuti akusonyezeni njira yoti muyendemo.+