Numeri 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma ana anu amene munati adzatengedwa ndi adani,+ amenewo ndi amene ndidzawalowetse mʼdzikolo ndipo adzadziwa dziko limene inu mwalikana.+ Deuteronomo 1:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Komanso ana anu amene munanena kuti adzagwidwa ndi adani,+ ana anu amene lero sakudziwa chabwino kapena choipa, amenewa ndi amene adzalowe mʼdzikolo ndipo ndidzawapatsa dzikolo kuti likhale lawo.+
31 Koma ana anu amene munati adzatengedwa ndi adani,+ amenewo ndi amene ndidzawalowetse mʼdzikolo ndipo adzadziwa dziko limene inu mwalikana.+
39 Komanso ana anu amene munanena kuti adzagwidwa ndi adani,+ ana anu amene lero sakudziwa chabwino kapena choipa, amenewa ndi amene adzalowe mʼdzikolo ndipo ndidzawapatsa dzikolo kuti likhale lawo.+