-
Numeri 26:63, 64Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
63 Awa ndi anthu amene Mose ndi wansembe Eleazara anawawerenga pakati pa Aisiraeli. Anawawerengera mʼchipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, kufupi ndi Yeriko. 64 Koma pakati pa anthu amenewa, panalibe munthu aliyense amene anali mʼgulu la anthu omwe anawerengedwa mʼchipululu cha Sinai, nthawi imene Mose ndi wansembe Aroni anawerenga Aisiraeli.+
-
-
Deuteronomo 1:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 ‘Palibe munthu ndi mmodzi yemwe mwa anthu a mʼbadwo woipa uwu amene adzaone dziko labwino limene ndinalumbira kuti ndidzalipereka kwa makolo anu,+
-
-
Salimo 95:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Choncho ndinalumbira nditakwiya kuti:
“Sadzalowa mumpumulo wanga.”+
-