-
Yoswa 14:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mose anandilumbirira tsiku limenelo kuti: ‘Dziko limene wakaliponda ndi mapazi ako lidzakhala cholowa chako ndi cha ana ako mpaka kalekale, chifukwa watsatira Yehova Mulungu wanga ndi mtima wako wonse.’+
-