-
Numeri 26:64Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
64 Koma pakati pa anthu amenewa, panalibe munthu aliyense amene anali mʼgulu la anthu omwe anawerengedwa mʼchipululu cha Sinai, nthawi imene Mose ndi wansembe Aroni anawerenga Aisiraeli.+
-
-
Deuteronomo 1:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 ‘Palibe munthu ndi mmodzi yemwe mwa anthu a mʼbadwo woipa uwu amene adzaone dziko labwino limene ndinalumbira kuti ndidzalipereka kwa makolo anu,+
-