-
Levitiko 26:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma ngati simudzandimvera kapena kutsatira malamulo onsewa,+
-
-
Deuteronomo 1:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Koma Yehova anandiuza kuti, ‘Auze kuti: “Musapite kukamenya nkhondo, chifukwa ine sindikhala nanu.+ Mukapita, adani anu akakugonjetsani.”’
-