-
Numeri 21:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Mfumu ya Akanani ya ku Aradi+ yomwe inkakhala ku Negebu itamva kuti Aisiraeli akubwera kudzera njira ya ku Atarimu, inapita kukamenyana nawo ndipo inagwira Aisiraeli ena nʼkupita nawo kudziko lake.
-
-
Deuteronomo 1:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Kenako Aamori amene ankakhala mʼphirimo anatuluka kudzakumana nanu ndipo anakuthamangitsani ngati mmene njuchi zimachitira, moti anakubalalitsani ku Seiri mpaka kukafika ku Horima.
-