Levitiko 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Levitiko 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Azipereka mbali ina ya nsembe yamgwirizanoyo ngati nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.+ Azipereka mafuta+ okuta matumbo ndi mafuta onse amene ali pamatumbo. Levitiko 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
3 Azipereka mbali ina ya nsembe yamgwirizanoyo ngati nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.+ Azipereka mafuta+ okuta matumbo ndi mafuta onse amene ali pamatumbo.