Ekisodo 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu amene adzachite zinthu modzikuza posamvera wansembe amene akutumikira Yehova Mulungu wanu kapena woweruza, ayenera kufa.+ Muzichotsa woipayo mu Isiraeli.+ Aheberi 10:26, 27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
12 Munthu amene adzachite zinthu modzikuza posamvera wansembe amene akutumikira Yehova Mulungu wanu kapena woweruza, ayenera kufa.+ Muzichotsa woipayo mu Isiraeli.+