- 
	                        
            
            Deuteronomo 5:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        13 Muzigwira ntchito zanu zonse masiku 6,+ 14 koma tsiku la 7 ndi sabata la Yehova Mulungu wanu.+ Musamagwire ntchito iliyonse,+ inuyo kapena mwana wanu wamwamuna, mwana wanu wamkazi, kapolo wanu wamwamuna, kapolo wanu wamkazi, ngʼombe yanu yamphongo, bulu wanu, chiweto chanu chilichonse, kapena mlendo amene akukhala mumzinda wanu,+ kuti nayenso kapolo wanu wamwamuna ndi kapolo wanu wamkazi, azipuma mofanana ndi inu.+ 
 
-