-
Levitiko 24:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 “Munthu wotemberera dzina la Mulungu uja, mupite naye kunja kwa msasa. Onse amene anamumva akutemberera aike manja awo pamutu pake ndipo gulu lonse limuponye miyala.+
-