Ekisodo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Numeri 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndodo ya munthu amene ndimusankheyo+ idzaphuka, ndipo ndidzathetsa kungʼungʼudza kwa Aisiraeli kumene akuchita motsutsana ndi ine+ komanso motsutsana ndi iwe.”+ Salimo 105:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno anatumiza Mose mtumiki wake,+Ndi Aroni+ amene anamusankha.
5 Ndodo ya munthu amene ndimusankheyo+ idzaphuka, ndipo ndidzathetsa kungʼungʼudza kwa Aisiraeli kumene akuchita motsutsana ndi ine+ komanso motsutsana ndi iwe.”+