-
Numeri 12:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndiyeno Yehova anatsika mʼchipilala chamtambo+ nʼkuima pakhomo la chihema chokumanako. Kenako anaitana Aroni ndi Miriamu ndipo onse anapita.
-