-
Numeri 16:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Aliyense adzatenge chofukizira chake nʼkuikamo zofukiza, ndipo aliyense adzabweretse chofukizira chake pamaso pa Yehova. Zofukizirazo zidzakhale zokwana 250, komanso iweyo ndi Aroni aliyense adzakhale ndi chake.”
-
-
Salimo 106:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Moto unayaka pakati pa gulu lawo.
Malawi amoto anapsereza oipa.+
-