-
Levitiko 7:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 “‘Lamulo la nsembe yakupalamula+ ndi ili: Nsembeyi ndi yopatulika koposa.
-
-
Levitiko 7:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Lamulo la nsembe yakupalamula ndi lofanana ndi la nsembe yamachimo. Nyama ya nsembeyi izikhala ya wansembe amene wapereka nsembeyo pophimba machimo.+
-