Ekisodo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Levitiko 27:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma munthu asapereke nyama iliyonse yoyamba kubadwa kuti ikhale yopatulika, chifukwa iliyonse yoyamba kubadwa ndi ya Yehova.+ Kaya ndi ngʼombe kapena nkhosa, ndi za Yehova.+ Numeri 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
26 Koma munthu asapereke nyama iliyonse yoyamba kubadwa kuti ikhale yopatulika, chifukwa iliyonse yoyamba kubadwa ndi ya Yehova.+ Kaya ndi ngʼombe kapena nkhosa, ndi za Yehova.+