-
2 Mbiri 31:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kuwonjezera pamenepo, Hezekiya anauza anthu a ku Yerusalemu kuti azipereka gawo loyenera kupita kwa ansembe ndi Alevi+ nʼcholinga choti iwo azitsatira mosamala lamulo la Yehova.
-