-
Numeri 13:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Iwo anabwerera kwa Mose ndi Aroni ndiponso gulu lonse la Aisiraeli mʼchipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera gulu lonselo za ulendo wawo nʼkuwaonetsa zipatso za kudzikolo.
-
-
Numeri 20:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Gulu lonse la Aisiraeli linanyamuka ku Kadesi kuja nʼkukafika kuphiri la Hora.+
-
-
Numeri 33:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Atanyamuka ku Ezioni-geberi anakamanga msasa mʼchipululu cha Zini,+ ku Kadesi.
-