Ekisodo 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Numeri 26:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Mkazi wa Amuramu anali Yokebedi,+ mwana wa Levi. Mkazi wa Levi anamuberekera mwana ameneyu ku Iguputo. Yokebedi anaberekera Amuramu ana awa: Aroni, Mose ndi mchemwali wawo Miriamu.+ Mika 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo,+Ndinakuwombolani mʼnyumba ya ukapolo,+Ndipo ndinakutumizirani Mose, Aroni ndi Miriamu kuti akutsogolereni.+
59 Mkazi wa Amuramu anali Yokebedi,+ mwana wa Levi. Mkazi wa Levi anamuberekera mwana ameneyu ku Iguputo. Yokebedi anaberekera Amuramu ana awa: Aroni, Mose ndi mchemwali wawo Miriamu.+
4 Ine ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo,+Ndinakuwombolani mʼnyumba ya ukapolo,+Ndipo ndinakutumizirani Mose, Aroni ndi Miriamu kuti akutsogolereni.+