- 
	                        
            
            Numeri 23:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        3 Ndiyeno Balamu anauza Balaki kuti: “Mukhale pompano pafupi ndi nsembe yanu yopsereza ndipo ine ndichoka. Mwina Yehova alankhula nane ndipo zimene andiuzezo ndikuuzani.” Choncho Balamu anapita pamwamba pa phiri. 
 
- 
                                        
- 
	                        
            
            Numeri 23:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        Panopa anthu anganene zokhudza Yakobo kapena kuti Isiraeli kuti: ‘Taonani zimene Mulungu wachita!’ 
 
-