- 
	                        
            
            Numeri 24:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        16 Mawu a munthu amene wamva mawu a Mulungu, Amene akudziwa Wamʼmwambamwamba, Anaona masomphenya a Wamphamvuyonse, Atagwada pansi, maso ake ali otsegula. Mawu ake akuti: 
 
-