Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mbiri 4:42, 43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Anthu ena a fuko la Simiyoni, amuna okwana 500, anapita kuphiri la Seiri+ ndipo amene ankawatsogolera anali Pelatiya, Neariya, Refaya ndi Uziyeli, ana a Isi. 43 Iwo anapha Aamaleki+ otsala omwe anathawa ndipo akukhala kumeneko mpaka lero.

  • Ezekieli 25:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 ‘Ine ndidzabwezera Edomu pogwiritsa ntchito anthu anga Aisiraeli.+ Aisiraeliwo adzachitira Edomu mogwirizana ndi mkwiyo komanso ukali wanga, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndikuwabwezera,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani