- 
	                        
            
            Ezekieli 27:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        6 Zopalasira zako anazipanga ndi mitengo ikuluikulu ya ku Basana, Ndipo mbali yakutsogolo kwako anaipanga ndi matabwa a paini, nʼkuikongoletsa ndi minyanga yochokera kuzilumba za Kitimu.+ 
 
-