-
Nahumu 3:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Abusa ako ayamba kuodzera, iwe mfumu ya Asuri,
Ndipo anthu ako olemekezeka akungokhala mʼnyumba zawo.
Anthu ako amwazikana mʼmapiri,
Ndipo palibe amene akuwasonkhanitsa.+
-