-
Numeri 22:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kenako Aisiraeli ananyamuka nʼkukamanga msasa mʼchipululu cha Mowabu, moyangʼanizana ndi Yeriko patsidya pa mtsinje wa Yorodano.+
-
-
Numeri 33:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Potsirizira pake ananyamuka kumapiri a Abarimu nʼkukamanga msasa ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, mʼchipululu cha Mowabu.+
-