-
Numeri 16:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Pambuyo pake, Mose anatuma munthu kuti akaitane Datani ndi Abiramu,+ ana a Eliyabu. Koma iwo anayankha kuti: “Ife sitibwerako kumeneko!
-