-
Deuteronomo 4:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Mukakweza maso anu kuthambo nʼkuona dzuwa, mwezi ndi nyenyezi, gulu lonse la zinthu zakuthambo, musakopeke nazo nʼkuyamba kuzigwadira komanso kuzitumikira.+ Yehova Mulungu wanu wazipereka kwa anthu onse okhala pansi pa thambo lonse.
-