-
Deuteronomo 11:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Onani, lero ndikuika dalitso ndi temberero pamaso panu:+
-
-
Deuteronomo 27:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 ‘Wotembereredwa ndi munthu amene sadzatsatira mawu a mʼChilamulo ichi ndipo sadzawagwiritsa ntchito.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’”)
-
-
Deuteronomo 28:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+
-