-
Numeri 26:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Amenewa anali mabanja a anthu a fuko la Rubeni ndipo amuna onse amene anawerengedwa analipo 43,730.+
-
-
Yoswa 13:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kenako Mose anagawira cholowa fuko la Rubeni motsatira mabanja awo.
-