-
Levitiko 26:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mudzakhala mukupuntha zimene mwakolola mpaka kufika nyengo yokolola mphesa, ndipo mudzakhala mukukolola mphesa mpaka kufika nyengo yofesa mbewu. Mudzadya mkate wanu nʼkukhuta, ndipo mudzakhala otetezeka mʼdziko lanu.+
-