-
1 Mafumu 4:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Anthu ochokera mʼmitundu yonse ankabwera kudzamva nzeru za Solomo, ngakhalenso mafumu onse apadziko lapansi amene anamva za nzeru zake.+
-
-
Danieli 1:19, 20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Mfumuyo italankhula nawo, inaona kuti pagulu lonselo panalibe aliyense amene ankafanana ndi Danieli, Hananiya, Misayeli ndi Azariya.+ Choncho anyamata amenewa anapitiriza kutumikira mfumu. 20 Pa nkhani iliyonse yofunika nzeru komanso kuzindikira, imene mfumu inkawafunsa, inaona kuti iwo anali anzeru kuwirikiza maulendo 10 kuposa ansembe onse ochita zamatsenga ndi anthu onse olankhula ndi mizimu+ amene anali mu ufumu wake wonse.
-