Hoseya 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwe unakhuta chifukwa unali ndi zakudya zambiri.+Unakhuta ndipo mtima wako unayamba kunyada. Choncho unandiiwala.+
6 Iwe unakhuta chifukwa unali ndi zakudya zambiri.+Unakhuta ndipo mtima wako unayamba kunyada. Choncho unandiiwala.+