Salimo 127:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Hoseya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye sanazindikire kuti ndine amene ndinkamupatsa mbewu,+ vinyo watsopano ndiponso mafuta.Sanazindikirenso kuti ndine amene ndinamupatsa siliva wambiri,Ndiponso golide amene anthu ankamugwiritsa ntchito polambira Baala.+
8 Iye sanazindikire kuti ndine amene ndinkamupatsa mbewu,+ vinyo watsopano ndiponso mafuta.Sanazindikirenso kuti ndine amene ndinamupatsa siliva wambiri,Ndiponso golide amene anthu ankamugwiritsa ntchito polambira Baala.+