-
Numeri 13:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Ngakhale zili choncho, anthu okhala kumeneko ndi anthu amphamvu zawo, ndipo ali ndi mizinda ikuluikulu yotchingidwa ndi mipanda yolimba kwambiri. Si zokhazo, taonanso Aanaki kumeneko.+
-