Deuteronomo 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi moto wowononga,+ iye ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.+ Aheberi 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
24 Chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi moto wowononga,+ iye ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.+