-
Deuteronomo 12:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Musamalambire Yehova Mulungu wanu mwa njira imeneyi, chifukwa iwo amachitira milungu yawo zinthu zonse zonyansa zimene Yehova amadana nazo. Iwo amafika ngakhale powotcha ana awo aamuna ndi aakazi pamoto kuti ikhale nsembe kwa milungu yawo.+
-
-
Deuteronomo 18:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mukakalowa mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, musakaphunzire kuchita zinthu zonyansa zimene anthu a mitundu yakumeneko akuchita.+
-