- 
	                        
            
            Deuteronomo 6:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
 - 
                            
- 
                                        
18 Muzichita zoyenera ndi zabwino pamaso pa Yehova kuti zikuyendereni bwino komanso kuti mukalowe mʼdziko labwino limene Yehova analumbira kwa makolo anu, nʼkulitenga kuti likhale lanu,+
 
 -